CLIMMA

Kampani ya Climma, ntchito yake ndikupanga ma Air-Conditioner ogwiritsa ntchito pamadzi komanso zipangizo zogwiritsa  ntchito pobweretsa mpweya wabwino mmadzi monga  pa nyanja ndi mmitsinje. Zinthu zomwe kampaniyi imapanga zimathandiza kuti katenthedwe ka mmadzi kadzibwelerera pa 360 degrees celcius omwe ndi mulingo woyenerera pa madzi

Available in