PIRELLI

Pireli and C ndi kampani yomwe imapapezeka mmayiko osiyanasiyana koma likulu lake liri ku Milan mdziko la italy. Kampaniyi yakhala ili pa mndandanda wa Stock Exchange ku Millan kuchokera mchaka cha 1922 ndipo mu 2015 kampani ya ChemChina inagula Pirelli and C.

Available in