Zaife

Saeed Mohammed Al Ghandi & Sons (SMAG) iyi ndi imodzi mwa dzina lodziwika bwino pa bizinesi ku liku ku Dubai, UAE.SMAG imapereka thandizo losiyana siyana monga kuperekera ma sipeya pati komanso kukonza. Zonsezi zimachitikira mmalo awo mutsogozedwa ndi akatswiri awo oposa 200. SMAG ndi nthambi ya AlGhandi Auto Group; UAE Automotive giants omwe amalemba anthu oposa 1000 mmadera osiyasiya ku GCC ndiponso East Africa. SMAG posachedwapa yatambasura manja ake poonjezera madera ena kupyora ku GCC, East Africa komanso ku Asia. Mmadera osewa kapaniyi imathandiza makasitomala ake kupyorera ka akadaulo odziwa ntchito. Chili chonse amapanga amaonetsetsa kuti ogula akusangalala nacho, chikuwapatsa mtendere ndiponso ndichotetezedwa bwino lomwe. Timaonetsetsanso kuti kudzera kwa akhala pakati athu zinthu zonse monga zomangira, ma basi, magalimoto a biziness kapena ongoyendera, ma taxi, zinthu zogwiritsa pa madzi, ma jenereta ndi zina zotero zizikhala zolimba komanso zoyenerera ndi momwe kapaniyi imafunira. 

Pansi pa nzeru, chilimbikinso ndi utsogoleri wa HE Saeed Mohammed Al Ghandi, Al Ghandi Auto Group, campaniyi ili ndi zitsamba zosonyeza ukadaulo wawo yochokera ku ISO 9001 ya Quality Management; ISO 14001 ya Environmental Management System, OHSAS 18001 potsatira Occupational health & safety, ISO10002 pa nkhani yodziwa kusamarila makasitomala ndiponso ISO 27001pa Information Security. Ma tsamba onsewa anaperekedwa kwa AlGhandi ataunikidwa kuti iwo amasata bwino nkhani zosamalira chilengedwe, kusamalira makasitomala awo powapangira zinthu zolimba ndiponso zowoneka bwino. Iwonso amatamandika chifukwa chakuyang’anira bwino ogwira ntchito awo powapasa malo abwino ogwirira ntchito.

Kampani ya Al Ghandi Auto Group inapangidwa ndi maso mphenya akuti Unite Arab Emirates ikhale patsogolo popanga zinthu za mtengo wapatali. A Ghandi Auto Group ali ndi cholinga chimodzi chomwe chili kukwanitsa cholinga chawo – kuwapatsa anthu mwayi kukawafikira  ndikulumikizana nawa, kuwapasa moyo wabwino powapangira katundu woti iwo azikhutira nayo ndiponso kuwathandiza akafuna chithandizo kwa ife pakatundu wawoyo. Ifetu timanyandira kugwira ntchito mosabisa kanthu and timafuna kuti onse amene amagwira ntchito zopanga, kutumiza kugulita ndiponso kukonza katundu wathu kuti tikhale nawo pau bale. Makulidwe akampaniyi ndi umboni wa nkhani nkhaniyi.

Tipezeni pa tsamba la intanet www.alghandi.com kuti muzionere nokh