IVECO TRAKKER AT380 T38H

Fomu yofunsira

Iyi ndi Thilaki yayikulu kwambiri ndipo imapezeka mmitundu yoposa 11,000 kuti ikwanire pa zofuna za makasitomala.

Iveco ndi kampani yayikulu kwambiri yomwe ili ndi  ma Thilaki ankhaninkhani komanso misika yambiri ndicholinga choti ma kasitomala ake azitha kuyipeza mosavuta. Kampaniyi imapezeka kwa mbiri mmayiko aku Africa komanso ku Middle East ndipo ili ndi galimoto za mtundu wa Thilaki zocheperapo,zapakatikati,zazikulu ndi zazikulu kwambiri. Padakali pano kampani-yi ikuyesetsabe kuti ikhale ndi misika yambiri ndi cholinga choti ma kasitonala ake asamavutike kugula. Pofika mchaka cha 2013 kukula kwa msikawu kumkayerekezedwa pa 230,000 units pofika mchaka cha 2013 womwe unali waukulu kwambiri poyerekeza ndi misika yaku Latin America  komanso ku Europe. Iveco ndi kampani imene  yakula modabwitsa kwambiri ndipo malonda ake akhala akukwera ndi 33% kuchokera mchaka cha 2010 kufika pa 12,000 units nchaka cha 2016. Iveco ikuyembekezekabe kupititsa patsogolo ntchito zake ndipo pofika mchaka cha 2018 ikuyembekezeka kukweza malonda ake kawiri kuposa mmene zikuyendera pano.Ntchito za Iveco zikuyembekezeka kukula chifukwa cha zifukwa zingapo:

 Choyamba  ndi chifukwa cha kapangidwe ka zinthu ka Kampani-yi,kufikira zofuna za ma kasitomala komanso kukulitsa ndikuchulukitsa misika ya kampani-yi. Gulu la loyendetsa kampani ya Iveco ku Africa ndi ku Middle East limalimbikitsa kwambiri ntchito yogulitsa,kupeza misika komanso kupanga ma ubale ndi makasitomala komanso ma kampani ena.Likulu la Iveco lomwe liri ku Turin limatsatsa malonda a zinthu zomwe kampaniyi imapanga,kuthandiza kupereka upangiri pakagwiritsidwe ntchito ka zinthu zomwe kampani-yi imapanga, komanso ili ndi gulu lomwe limapanga galimoto komanso zipangizo zina moyenerana ndi zomwe anthu akufuna.

المواصفات :

  • Capacity : 12.88 litres
  • Engine : Iveco Cursor 13 Turbocharger + Waste-Gate valve
  • Gearbox : EUROTRONIC/ MECHANICAL
  • Suspension : Front - Parabolic leaf / Optional Semi Elliptical; Rear - Semielliptic leaf; Anti roll bar - Front & 1st rear; Shock absorbers - 2 on front
  • Type : 6x4 chassis cab